-
Maliko 9:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Ndiye Petulo anauza Yesu kuti: “Rabi, zingakhale bwino ife titamakhala pano. Choncho timange matenti atatu pano, imodzi yanu, imodzi ya Mose ndi ina ya Eliya.”
-