Maliko 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno kunachita mtambo umene unawaphimba. Kenako panamveka mawu+ kuchokera mumtambomo akuti: “Uyu ndi Mwana wanga wokondedwa.+ Muzimumvera.”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:7 Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu,5/2018, tsa. 4
7 Ndiyeno kunachita mtambo umene unawaphimba. Kenako panamveka mawu+ kuchokera mumtambomo akuti: “Uyu ndi Mwana wanga wokondedwa.+ Muzimumvera.”+