Maliko 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamene ankatsika mʼphirimo, Yesu anawalamula mwamphamvu kuti asauze aliyense zimene anaonazo,+ mpaka Mwana wa munthu atauka kwa akufa.+
9 Pamene ankatsika mʼphirimo, Yesu anawalamula mwamphamvu kuti asauze aliyense zimene anaonazo,+ mpaka Mwana wa munthu atauka kwa akufa.+