Maliko 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iye anawayankha kuti: “Eliya adzabweradi choyamba nʼkubwezeretsa zinthu zonse.+ Koma nʼchifukwa chiyani malemba amanena kuti Mwana wa munthu ayenera kukumana ndi mavuto ambiri+ komanso kumuchitira zinthu zachipongwe?+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:12 Nsanja ya Olonda,7/1/1989, tsa. 30
12 Iye anawayankha kuti: “Eliya adzabweradi choyamba nʼkubwezeretsa zinthu zonse.+ Koma nʼchifukwa chiyani malemba amanena kuti Mwana wa munthu ayenera kukumana ndi mavuto ambiri+ komanso kumuchitira zinthu zachipongwe?+