Maliko 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Atayandikira kumene kunali ophunzira ena aja, iwo anaona gulu lalikulu la anthu litawazungulira ndipo panali alembi amene ankakangana nawo.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:14 Yesu—Ndi Njira, tsa. 146 Nsanja ya Olonda,1/15/1988, tsa. 8
14 Atayandikira kumene kunali ophunzira ena aja, iwo anaona gulu lalikulu la anthu litawazungulira ndipo panali alembi amene ankakangana nawo.+