Maliko 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Munthu wina amene anali mʼgululo anamuyankha kuti: “Mphunzitsi, ine ndabweretsa mwana wanga wamwamuna kwa inu chifukwa ali ndi mzimu umene umamulepheretsa kulankhula.+
17 Munthu wina amene anali mʼgululo anamuyankha kuti: “Mphunzitsi, ine ndabweretsa mwana wanga wamwamuna kwa inu chifukwa ali ndi mzimu umene umamulepheretsa kulankhula.+