-
Maliko 9:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Choncho iwo anapita naye kwa Yesu. Koma mzimuwo utamuona, nthawi yomweyo unachititsa kuti mwanayo aphuphe. Anagwa pansi nʼkumagubudukagubuduka ndipo ankachita thovu kukamwa.
-