-
Maliko 9:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 ndipo nthawi zambiri umamugwetsera pamoto komanso mʼmadzi kuti umuwononge. Koma ngati mungathe kuchitapo kanthu, tichitireni chifundo nʼkutithandiza.”
-