Maliko 9:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Tsopano Yesu ataona kuti gulu la anthu likuthamangira kwa iwo, anakalipira mzimu wonyansawo kuti: “Iwe mzimu wolepheretsa munthu kulankhula komanso kumva, ndikukulamula, tuluka ndipo usadzalowenso mwa iye.”+
25 Tsopano Yesu ataona kuti gulu la anthu likuthamangira kwa iwo, anakalipira mzimu wonyansawo kuti: “Iwe mzimu wolepheretsa munthu kulankhula komanso kumva, ndikukulamula, tuluka ndipo usadzalowenso mwa iye.”+