Maliko 9:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno atalowa mʼnyumba, ophunzira ake anamufunsa ali kwaokha kuti: “Nʼchifukwa chiyani ife tinalephera kutulutsa chiwanda chija?”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:28 Yesu—Ndi Njira, tsa. 147 Nsanja ya Olonda,1/15/1988, tsa. 8
28 Ndiyeno atalowa mʼnyumba, ophunzira ake anamufunsa ali kwaokha kuti: “Nʼchifukwa chiyani ife tinalephera kutulutsa chiwanda chija?”+