Maliko 9:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Chifukwa iye ankaphunzitsa ophunzira ake nʼkuwauza kuti: “Mwana wa munthu adzaperekedwa mʼmanja mwa anthu ndipo adzamupha.+ Koma ngakhale adzamuphe, adzauka patatha masiku atatu.”+
31 Chifukwa iye ankaphunzitsa ophunzira ake nʼkuwauza kuti: “Mwana wa munthu adzaperekedwa mʼmanja mwa anthu ndipo adzamupha.+ Koma ngakhale adzamuphe, adzauka patatha masiku atatu.”+