Maliko 9:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Choncho anakhala pansi nʼkuitana ophunzira 12 aja nʼkuwauza kuti: “Ngati aliyense akufuna kukhala woyamba, ayenera kukhala wotsiriza pa onse ndiponso mtumiki wa onse.”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:35 Nsanja ya Olonda,2/1/2007, ptsa. 8-9
35 Choncho anakhala pansi nʼkuitana ophunzira 12 aja nʼkuwauza kuti: “Ngati aliyense akufuna kukhala woyamba, ayenera kukhala wotsiriza pa onse ndiponso mtumiki wa onse.”+