Maliko 9:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Kenako Yohane anauza Yesu kuti: “Mphunzitsi, ife tinaona munthu wina akutulutsa ziwanda mʼdzina lanu ndiye tinamuletsa, chifukwa sakuyenda ndi ife.”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:38 Yesu—Ndi Njira, tsa. 150 Nsanja ya Olonda,2/15/1988, tsa. 8
38 Kenako Yohane anauza Yesu kuti: “Mphunzitsi, ife tinaona munthu wina akutulutsa ziwanda mʼdzina lanu ndiye tinamuletsa, chifukwa sakuyenda ndi ife.”+