Maliko 9:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Komanso aliyense amene wakupatsani kapu ya madzi akumwa chifukwa chakuti ndinu ophunzira a Khristu,+ ndithu ndikukuuzani, ameneyo mphoto yake sidzatayika.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:41 Yesu—Ndi Njira, tsa. 150 Nsanja ya Olonda,2/15/1988, tsa. 8
41 Komanso aliyense amene wakupatsani kapu ya madzi akumwa chifukwa chakuti ndinu ophunzira a Khristu,+ ndithu ndikukuuzani, ameneyo mphoto yake sidzatayika.+