Maliko 9:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Mchere ndi wabwino, koma ngati mcherewo watha mphamvu, kodi mphamvuyo mungaibwezeretse bwanji?+ Khalani ndi mchere mwa inu nokha+ ndipo sungani mtendere pakati panu.”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:50 Yesu—Ndi Njira, tsa. 151 Nsanja ya Olonda,2/15/1988, tsa. 9
50 Mchere ndi wabwino, koma ngati mcherewo watha mphamvu, kodi mphamvuyo mungaibwezeretse bwanji?+ Khalani ndi mchere mwa inu nokha+ ndipo sungani mtendere pakati panu.”+