Maliko 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Atachoka kumeneko anapita kumalire a Yudeya kutsidya lina la Yorodano. Kumenekonso gulu la anthu linasonkhana kwa iye. Mwachizolowezi chake Yesu anayambanso kuwaphunzitsa.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:1 Yesu—Ndi Njira, tsa. 222 Nsanja ya Olonda,7/15/1989, tsa. 8
10 Atachoka kumeneko anapita kumalire a Yudeya kutsidya lina la Yorodano. Kumenekonso gulu la anthu linasonkhana kwa iye. Mwachizolowezi chake Yesu anayambanso kuwaphunzitsa.+