Maliko 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iwe umadziwa malamulo akuti: ‘Musaphe munthu,*+ musachite chigololo,+ musabe,+ musapereke umboni wabodza,+ musabere munthu mwachinyengo+ ndiponso lakuti muzilemekeza bambo anu ndi mayi anu.’”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:19 Nsanja ya Olonda,6/15/1986, ptsa. 8-9
19 Iwe umadziwa malamulo akuti: ‘Musaphe munthu,*+ musachite chigololo,+ musabe,+ musapereke umboni wabodza,+ musabere munthu mwachinyengo+ ndiponso lakuti muzilemekeza bambo anu ndi mayi anu.’”+