-
Maliko 10:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Koma ophunzirawo anadabwa ndi mawu akewa. Ndiyeno Yesu anawauza kuti: “Ana inu, kulowa mu Ufumu wa Mulungu nʼkovuta kwambiri!
-