Maliko 10:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yesu anawayangʼanitsitsa nʼkuwauza kuti: “Kwa anthu zimenezi nʼzosatheka, koma sizili choncho kwa Mulungu chifukwa zinthu zonse nʼzotheka kwa Mulungu.”+
27 Yesu anawayangʼanitsitsa nʼkuwauza kuti: “Kwa anthu zimenezi nʼzosatheka, koma sizili choncho kwa Mulungu chifukwa zinthu zonse nʼzotheka kwa Mulungu.”+