Maliko 10:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Petulo anayamba kumuuza kuti: “Taonani! Ife tasiya zinthu zonse nʼkukutsatirani.”+