Maliko 10:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndiyeno Yakobo ndi Yohane, ana aamuna a Zebedayo,+ anapita kwa iye nʼkumuuza kuti: “Mphunzitsi, tikufuna kuti mutichitire chilichonse chimene tingakupempheni.”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:35 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 228-229 Nsanja ya Olonda,9/1/1989, tsa. 8 Mawu a Mulungu, tsa. 89
35 Ndiyeno Yakobo ndi Yohane, ana aamuna a Zebedayo,+ anapita kwa iye nʼkumuuza kuti: “Mphunzitsi, tikufuna kuti mutichitire chilichonse chimene tingakupempheni.”+