-
Maliko 10:40Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
40 Koma si ine woyenera kusankha amene adzakhale kudzanja langa lamanja kapena lamanzere. Atate wanga adzapereka mwayi umenewo kwa anthu amene anawakonzera.”
-