Maliko 10:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Koma Yesu anawaitana nʼkuwauza kuti: “Inu mukudziwa kuti amene amaoneka ngati* akulamulira anthu a mitundu ina, amapondereza anthu awo ndipo akuluakulu awo amasonyeza mphamvu zawo pa iwo.+
42 Koma Yesu anawaitana nʼkuwauza kuti: “Inu mukudziwa kuti amene amaoneka ngati* akulamulira anthu a mitundu ina, amapondereza anthu awo ndipo akuluakulu awo amasonyeza mphamvu zawo pa iwo.+