Maliko 10:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Kenako anafika ku Yeriko. Koma pamene iye ndi ophunzira ake komanso gulu lalikulu ndithu ankatuluka mu Yeriko, Batimeyu (mwana wa Timeyu) wopemphapempha amene anali ndi vuto losaona, anakhala pansi mʼmphepete mwa msewu.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:46 Yesu—Ndi Njira, tsa. 230 Nsanja ya Olonda,5/1/2008, tsa. 319/15/1989, tsa. 82/1/1988, tsa. 5
46 Kenako anafika ku Yeriko. Koma pamene iye ndi ophunzira ake komanso gulu lalikulu ndithu ankatuluka mu Yeriko, Batimeyu (mwana wa Timeyu) wopemphapempha amene anali ndi vuto losaona, anakhala pansi mʼmphepete mwa msewu.+