Maliko 10:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Atamva kuti Yesu Mnazareti akudutsa, Batimeyu anayamba kufuula kuti: “Yesu, Mwana wa Davide,+ ndichitireni chifundo!”+
47 Atamva kuti Yesu Mnazareti akudutsa, Batimeyu anayamba kufuula kuti: “Yesu, Mwana wa Davide,+ ndichitireni chifundo!”+