-
Maliko 10:48Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
48 Atatero anthu ambiri anayamba kumudzudzula nʼkumamuuza kuti akhale chete. Koma akatero mʼpamenenso iye ankafuula kwambiri kuti: “Mwana wa Davide, ndichitireni chifundo!”
-