-
Maliko 11:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Iye anawauza kuti: “Pitani mʼmudzi umene mukuuonawo ndipo mukakangolowa mmenemo, mukapeza bulu wamngʼono wamphongo atamumangirira, amene munthu sanakwerepo chiyambire. Mukamumasule nʼkubwera naye kuno.
-