Maliko 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho iwo ananyamuka ndipo anapezadi bulu wamphongo atamumangirira pakhomo, mʼmphepete mwa msewu waungʼono. Ndipo iwo anamasula buluyo.+
4 Choncho iwo ananyamuka ndipo anapezadi bulu wamphongo atamumangirira pakhomo, mʼmphepete mwa msewu waungʼono. Ndipo iwo anamasula buluyo.+