Maliko 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthuwo anabweretsa bulu uja+ kwa Yesu. Kenako anayala malaya awo akunja pabuluyo ndipo iye anakwerapo.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:7 Yesu—Ndi Njira, tsa. 238 Nsanja ya Olonda,11/1/1989, tsa. 8
7 Anthuwo anabweretsa bulu uja+ kwa Yesu. Kenako anayala malaya awo akunja pabuluyo ndipo iye anakwerapo.+