Maliko 11:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Komanso anthu ambiri anayala malaya awo akunja mumsewu ndipo ena anadula masamba mʼminda.+