Maliko 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iye analowa mu Yerusalemu nʼkufika mʼkachisi. Ndiyeno anayangʼanayangʼana zinthu zonse, koma popeza nthawi inali itatha kale, anapita ku Betaniya limodzi ndi ophunzira ake 12 aja.+
11 Iye analowa mu Yerusalemu nʼkufika mʼkachisi. Ndiyeno anayangʼanayangʼana zinthu zonse, koma popeza nthawi inali itatha kale, anapita ku Betaniya limodzi ndi ophunzira ake 12 aja.+