Maliko 11:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ansembe aakulu ndi alembi anamva zimenezo, ndipo anayamba kufunafuna njira yoti amuphere+ chifukwa ankamuopa popeza gulu lonse la anthu linkadabwa ndi zimene ankaphunzitsa.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:18 Yesu—Ndi Njira, tsa. 240 Nsanja ya Olonda,11/15/1989, tsa. 8
18 Ansembe aakulu ndi alembi anamva zimenezo, ndipo anayamba kufunafuna njira yoti amuphere+ chifukwa ankamuopa popeza gulu lonse la anthu linkadabwa ndi zimene ankaphunzitsa.+