Maliko 11:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho Petulo, anaukumbukira ndipo ananena kuti: “Rabi, taonani! Mtengo wamkuyu umene munautemberera uja wafota.”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:21 Yesu—Ndi Njira, tsa. 244
21 Choncho Petulo, anaukumbukira ndipo ananena kuti: “Rabi, taonani! Mtengo wamkuyu umene munautemberera uja wafota.”+