Maliko 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndithu ndikukuuzani kuti aliyense wouza phiri ili kuti, ‘Nyamuka pano ukadziponye mʼnyanja,’ ndipo sakukayikira mumtima mwake koma ali ndi chikhulupiriro kuti zimene wanena zichitikadi, zidzaterodi.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:23 Yesu—Ndi Njira, tsa. 244 Nsanja ya Olonda,12/15/1989, tsa. 8
23 Ndithu ndikukuuzani kuti aliyense wouza phiri ili kuti, ‘Nyamuka pano ukadziponye mʼnyanja,’ ndipo sakukayikira mumtima mwake koma ali ndi chikhulupiriro kuti zimene wanena zichitikadi, zidzaterodi.+