Maliko 11:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Nʼchifukwa chake ndikukuuzani kuti, zinthu zonse zimene mukupempha ndi kuzipempherera, muzikhulupirira kuti mwazilandira kale ndipo mudzazilandiradi.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:24 Kufotokoza Mavesi a m’Baibulo, article 35
24 Nʼchifukwa chake ndikukuuzani kuti, zinthu zonse zimene mukupempha ndi kuzipempherera, muzikhulupirira kuti mwazilandira kale ndipo mudzazilandiradi.+