-
Maliko 11:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Yesu anawayankha kuti: “Ndikufunsani funso limodzi. Mundiyankhe, ndipo inenso ndikuuzani amene anandipatsa ulamuliro umene ndimachitira zimenezi.
-