-
Maliko 11:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Choncho iwo anayamba kukambirana kuti: “Tikanena kuti, ‘Unachokera kumwamba,’ atifunsa kuti, ‘Nanga nʼchifukwa chiyani simunamukhulupirire?’
-