Maliko 11:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Koma tinganene kuti ‘Unachokera kwa anthuʼ ngati?” Iwo ankaopa gulu la anthu, chifukwa anthu onsewo ankakhulupirira kuti Yohane analidi mneneri.+
32 Koma tinganene kuti ‘Unachokera kwa anthuʼ ngati?” Iwo ankaopa gulu la anthu, chifukwa anthu onsewo ankakhulupirira kuti Yohane analidi mneneri.+