Maliko 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye anatsala ndi mmodzi yekha woti amutumize, mwana wake wokondedwa.+ Choncho anamutumizadi nʼkunena kuti, ‘Mwana wanga yekhayu akamulemekeza.’
6 Iye anatsala ndi mmodzi yekha woti amutumize, mwana wake wokondedwa.+ Choncho anamutumizadi nʼkunena kuti, ‘Mwana wanga yekhayu akamulemekeza.’