Maliko 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Atamva zimenezo ankafuna kumugwira,* koma anaopa gulu la anthu, chifukwa iwo anadziwa kuti iye ananena fanizolo akuganiza za iwowo. Choncho anangomusiya nʼkuchokapo.+
12 Atamva zimenezo ankafuna kumugwira,* koma anaopa gulu la anthu, chifukwa iwo anadziwa kuti iye ananena fanizolo akuganiza za iwowo. Choncho anangomusiya nʼkuchokapo.+