Maliko 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pambuyo pake anamutumizira ena mwa Afarisi ndi anthu amene ankatsatira Herode kuti akamupezere zifukwa pa zimene angalankhule.+
13 Pambuyo pake anamutumizira ena mwa Afarisi ndi anthu amene ankatsatira Herode kuti akamupezere zifukwa pa zimene angalankhule.+