-
Maliko 12:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Iwo anamubweretsera ndipo iye anawafunsa kuti: “Kodi nkhope iyi komanso mawu akewa nʼzandani?” Iwo anayankha kuti: “Ndi za Kaisara.”
-