Maliko 12:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Mphunzitsi, Mose anatilembera kuti ngati mwamuna wamwalira nʼkusiya mkazi koma osasiya mwana, mchimwene wake akuyenera kutenga mkazi wamasiyeyo nʼkuberekera mchimwene wake uja ana.+
19 “Mphunzitsi, Mose anatilembera kuti ngati mwamuna wamwalira nʼkusiya mkazi koma osasiya mwana, mchimwene wake akuyenera kutenga mkazi wamasiyeyo nʼkuberekera mchimwene wake uja ana.+