Maliko 12:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mmodzi wa alembi amene anafika nʼkuwamva akutsutsana, anadziwa kuti anawayankha bwino. Choncho anafunsa Yesu kuti: “Kodi lamulo loyamba* ndi liti pa malamulo onse?”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:28 Nsanja ya Olonda,3/1/2013, tsa. 13
28 Mmodzi wa alembi amene anafika nʼkuwamva akutsutsana, anadziwa kuti anawayankha bwino. Choncho anafunsa Yesu kuti: “Kodi lamulo loyamba* ndi liti pa malamulo onse?”+