Maliko 12:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Yesu atazindikira kuti mlembiyo wayankha mwanzeru, anamuuza kuti: “Iwe suli kutali ndi Ufumu wa Mulungu.” Koma panalibe amene analimba mtima kuti amufunsenso.+
34 Yesu atazindikira kuti mlembiyo wayankha mwanzeru, anamuuza kuti: “Iwe suli kutali ndi Ufumu wa Mulungu.” Koma panalibe amene analimba mtima kuti amufunsenso.+