Maliko 12:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Davideyo anamutchula kuti Ambuye, ndiye zingatheke bwanji kuti akhale mwana wake?”+ Ndipo gulu lalikulu la anthu linkamumvetsera mosangalala. Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:37 Yesu—Ndi Njira, tsa. 252 Nsanja ya Olonda,2/15/1990, tsa. 8
37 Davideyo anamutchula kuti Ambuye, ndiye zingatheke bwanji kuti akhale mwana wake?”+ Ndipo gulu lalikulu la anthu linkamumvetsera mosangalala.