Maliko 12:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Pophunzitsapo Yesu ananenanso kuti: “Chenjerani ndi alembi amene amakonda kuyendayenda atavala mikanjo komanso amakonda kupatsidwa moni mʼmisika.+
38 Pophunzitsapo Yesu ananenanso kuti: “Chenjerani ndi alembi amene amakonda kuyendayenda atavala mikanjo komanso amakonda kupatsidwa moni mʼmisika.+