Maliko 12:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ndiyeno anakhala pansi pamalo amene ankatha kuona moponyeramo zopereka*+ ndipo anayamba kuona mmene gulu la anthu linkaponyera ndalama moponyera zoperekamo. Anaona anthu ambiri olemera akuponyamo makobidi ambiri.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:41 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),4/2021, tsa. 6 Nsanja ya Olonda,12/1/1987, tsa. 28
41 Ndiyeno anakhala pansi pamalo amene ankatha kuona moponyeramo zopereka*+ ndipo anayamba kuona mmene gulu la anthu linkaponyera ndalama moponyera zoperekamo. Anaona anthu ambiri olemera akuponyamo makobidi ambiri.+