Maliko 12:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Ndiyeno Yesu anaitana ophunzira ake nʼkuwauza kuti: “Ndithu ndikukuuzani kuti mkazi wamasiye wosaukayu waponya zochuluka kuposa ena onse amene aponya ndalama moponyera zoperekamo.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:43 Yandikirani, ptsa. 184-185 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),4/2021, tsa. 6 Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu,5/2018, tsa. 5 Nsanja ya Olonda,10/15/1997, tsa. 17
43 Ndiyeno Yesu anaitana ophunzira ake nʼkuwauza kuti: “Ndithu ndikukuuzani kuti mkazi wamasiye wosaukayu waponya zochuluka kuposa ena onse amene aponya ndalama moponyera zoperekamo.+
12:43 Yandikirani, ptsa. 184-185 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),4/2021, tsa. 6 Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu,5/2018, tsa. 5 Nsanja ya Olonda,10/15/1997, tsa. 17