Maliko 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yesu akutuluka mʼkachisi, mmodzi wa ophunzira ake anamuuza kuti: “Mphunzitsi, taonani mmene miyala ndi nyumbazi zikukongolera!”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:1 Yesu—Ndi Njira, tsa. 255 Galamukani!,9/2009, tsa. 26 Nsanja ya Olonda,3/1/1990, tsa. 25
13 Yesu akutuluka mʼkachisi, mmodzi wa ophunzira ake anamuuza kuti: “Mphunzitsi, taonani mmene miyala ndi nyumbazi zikukongolera!”+